Mwazi wa Yesu lyrics
Songs
2025-12-16 19:48:54
Mwazi wa Yesu lyrics
Mwazi wa Yesu, mwazi wa Yesu ndaima,
iwe Satana, sungachite, ndaima
Mwazi wa Yesu, mwazi wa Yesu ndaima,
iwe oipa, sungachite, ndaima
- Artist:Malawi Folk