Angathe [English translation]
Songs
2024-12-23 21:40:44
Angathe [English translation]
Ulemerero wanu
Ukhale nthawi zonse
Ambuye!
Kondwerani ndi ntchito ya manja anu.
Munalenga munthu
Mu chifaniziro chanu
Ambuye!
Kondwerani ndi ntchito ya manja anu.
Ndidza
Kuimbirani ine ndikadali ndi moyo,
Ndidzalemekeza ‘Nu ndi umunthu wanga wonse.
Mulungu
Angathe x 5
Angathe Mulungu angathe salephera!
Ndiye Alefa – Omega
Woyamba – Wotsiriza
Wachipulumutso cha moyo wanga;
Mulungu angathe, angathe, angathe
Mulungu angathe salephera.
- Artist:Malawi Folk