Ndinu Woyera lyrics
Songs
2025-01-10 12:19:54
Ndinu Woyera lyrics
Ndinu woyera (x3)
Yesu, Ambuye ndinu woyera.
Ambuye ndinu munali
Ndinu munali
Ndipo Muli
Ndipo mudzakhala kunthawi zosatha
Ndinu woyera
Ambuye palibe wina
Palibe wina koposa inu
Palibe wina angakhale nanu
Ndinu woyera Yesu
- Artist:Malawi Folk