Palibe amene angafanane naye [English translation]
Songs
2024-12-24 13:25:38
Palibe amene angafanane naye [English translation]
Palibe amene angafanane naye (x2 )
Mfumu ya mafumu.
Kalonga wa mtendere,
Palibe amene angafanane naye.
Asowa amene angafanane naye (x2)
Mfumu ya mafumu.
Kalonga wa mtendere,
Asowa amene angafanane naye
Muyangane chilengedwe nchito ya manja anu (x2)
Mfumu ya mafumu.
Kalonga wa mtendere,
Muyangane chilengedwe nchito ya manja anu
Dzina lanu ndi lipambana Ambuye
Dzina lanu ndi la mphamvu Ambuye
How wonderful is your name
- Artist:Malawi Folk