Palibe wofana naye [English translation]
Songs
2026-07-11 15:06:09
Palibe wofana naye [English translation]
Palibe wofana naye (x3)
Sadzapezekanso
Ndayenda,
Ndayendayenda ponse, ponse
Ndazungulira konse, konse
Ndafunafuna konse, konse
Sadzapezekanso
- Artist:Malawi Folk