Yesu Wanga lyrics
Songs
2026-01-31 08:52:23
Yesu Wanga lyrics
Yesu wanga wondisamalira ine
Yesu wanga wondisamala (x2)
Suyo! Yesu wanga
Wanditulutsa, wandisambitsa ine;
Wanditulutsa, wandisambitsa,
Wandiyeretsa, wandikwezeka
Suyo! Yesu wanga.
- Artist:Malawi Folk